Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 19:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 anthu awiri amene akukanganawo aziima pamaso pa Yehova, kapena kuti pamaso pa ansembe ndi oweruza amene akuweruza masiku amenewo.+

  • Deuteronomo 21:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ansembe, omwe ndi Alevi, azifika pafupi chifukwa ndi amene Yehova Mulungu wanu wawasankha kuti azimutumikira+ komanso azidalitsa mʼdzina la Yehova.+ Iwo ndi amene akuyenera kunena njira yothetsera mkangano uliwonse wokhudza zinthu zankhanza zimene zachitika.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani