22 Mukasunga mosamala malamulo onsewa amene ndikukupatsani nʼkumawatsatira, kukonda Yehova Mulungu wanu,+ kuyenda mʼnjira zake zonse ndi kumʼmamatira,+ 23 Yehova adzathamangitsa mitundu yonseyi pamaso panu,+ ndipo mitundu yamphamvu ndi yaikulu kuposa inu mudzailanda dziko.+