-
Deuteronomo 13:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 muzifufuza mosamala kwambiri komanso muzifunsa ena za nkhaniyo.+ Ndiye zikatsimikizirika kuti ndi zoonadi kuti chinthu chonyansachi chachitika pakati panu,
-
-
2 Mbiri 19:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndiyeno anauza oweruzawo kuti: “Muzichita zinthu mosamala chifukwa simukuweruzira munthu koma Yehova, ndipo iye ali nanu pa ntchito yoweruzayi.+
-