Levitiko 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Levitiko 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwamuna amene wagona ndi mkazi wa bambo ake, wachititsa manyazi* bambo akewo.+ Mwamuna ndi mkaziyo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo uzikhala pa iwo. Deuteronomo 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mkazi wa bambo ake, chifukwa wachititsa manyazi bambo akewo.’*+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’) 1 Akorinto 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
11 Mwamuna amene wagona ndi mkazi wa bambo ake, wachititsa manyazi* bambo akewo.+ Mwamuna ndi mkaziyo aziphedwa ndithu. Mlandu wa magazi awo uzikhala pa iwo.
20 ‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mkazi wa bambo ake, chifukwa wachititsa manyazi bambo akewo.’*+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)