-
Numeri 23:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Atatero Balaki anauza Balamu kuti: “Ngati simungathe kuwatemberera ngakhale pangʼono, ndiye musawadalitsenso.”
-
-
Numeri 24:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako Balaki anapsera mtima Balamu. Ndiyeno Balaki anawomba mʼmanja mokwiya nʼkuuza Balamu kuti: “Ndinakuitana kuti udzatemberere adani anga,+ koma iwe wawadalitsa kwambiri maulendo atatu onsewa.
-