-
Deuteronomo 15:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Pakati panu pasapezeke munthu wosauka, chifukwa Yehova adzakudalitsani ndithu+ mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale cholowa chanu.
-
-
Deuteronomo 15:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ngati mmodzi mwa abale anu wasauka pakati panu, mu umodzi mwa mizinda yanu mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, musamamuumire mtima kapena kumuumitsira dzanja lanu.+
-