Ekisodo 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Levitiko 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Numeri 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Numeri 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndakupatsa+ mafuta onse abwino koposa, vinyo yense watsopano wabwino koposa ndi mbewu zabwino koposa, zimenezi ndi zipatso zawo zoyambirira+ zimene azipereka kwa Yehova. 2 Mbiri 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ndasankha Yerusalemu+ kuti dzina langa likhale kumeneko ndiponso ndasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’+ 2 Mbiri 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aisiraeli atangomva zimenezi, anapereka zinthu zambiri zoyambirira kukolola monga mbewu, vinyo watsopano, mafuta,+ uchi ndi zokolola zonse zakumunda+ ndipo anapereka mowolowa manja chakhumi cha zinthu zonse.+ Miyambo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
12 Ndakupatsa+ mafuta onse abwino koposa, vinyo yense watsopano wabwino koposa ndi mbewu zabwino koposa, zimenezi ndi zipatso zawo zoyambirira+ zimene azipereka kwa Yehova.
6 Koma ndasankha Yerusalemu+ kuti dzina langa likhale kumeneko ndiponso ndasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’+
5 Aisiraeli atangomva zimenezi, anapereka zinthu zambiri zoyambirira kukolola monga mbewu, vinyo watsopano, mafuta,+ uchi ndi zokolola zonse zakumunda+ ndipo anapereka mowolowa manja chakhumi cha zinthu zonse.+