-
Levitiko 26:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma ngati simudzandimvera kapena kutsatira malamulo onsewa,+
-
-
1 Samueli 4:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho Afilisiti anamenyadi nkhondo ndipo Aisiraeli anagonja+ moti aliyense anathawira kutenti yake. Aisiraeli amene anaphedwa anali ambiri. Panaphedwa asilikali oyenda pansi okwana 30,000.
-