Zefaniya 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chuma chawo chidzatengedwa ndipo nyumba zawo zidzawonongedwa.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wake.+
13 Chuma chawo chidzatengedwa ndipo nyumba zawo zidzawonongedwa.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wake.+