Yeremiya 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Taonani! Mdani adzabwera ngati mitambo yamvula,Ndipo magaleta ake ali ngati mphepo yamkuntho.+ Mahatchi ake ndi aliwiro kuposa ziwombankhanga.+ Tsoka latigwera chifukwa tawonongedwa. Hoseya 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
13 Taonani! Mdani adzabwera ngati mitambo yamvula,Ndipo magaleta ake ali ngati mphepo yamkuntho.+ Mahatchi ake ndi aliwiro kuposa ziwombankhanga.+ Tsoka latigwera chifukwa tawonongedwa.