Ekisodo 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 31:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Tengani buku ili la Chilamulo+ ndipo muliike pambali pa likasa+ la pangano la Yehova Mulungu wanu, ndipo lidzakhala mboni ya Mulungu yokutsutsani.
26 “Tengani buku ili la Chilamulo+ ndipo muliike pambali pa likasa+ la pangano la Yehova Mulungu wanu, ndipo lidzakhala mboni ya Mulungu yokutsutsani.