-
Deuteronomo 20:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Mukayandikira mzinda kuti mumenyane nawo, muzilengeza kwa anthu amumzindawo mfundo za mtendere.+
-
-
Deuteronomo 20:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Muzichita zimenezi ndi mizinda yonse imene ili kutali kwambiri ndi inu, yomwe sili pakati pa mizinda ya mitundu iyi imene yayandikana nanu.
-