-
Oweruza 16:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno Delila anatenga zingwe zatsopano nʼkumumanga nazo manja ndipo anamuuza kuti: “Afilisiti aja abwera Samisoni!” (Pa nthawiyi nʼkuti anthu atamʼbisalira mʼchipinda china.) Samisoni atamva zimenezi anadula zingwe zimene anamʼmanga nazozo ngati akudula ulusi.+
-
-
Oweruza 16:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Iye anamangadi zingongozo nʼkuzipina. Kenako anamuuza kuti: “Afilisiti aja abwera Samisoni!” Samisoni atamva zimenezi anadzuka ndipo anachotsa chopinira chija komanso ulusi uja.
-