Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Deuteronomo 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Inuyo mwasonyezedwa zinthu zimenezi kuti mudziwe kuti Yehova ndi Mulungu woona.+ Palibenso Mulungu wina kupatulapo iyeyo.+ Salimo 73:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 86:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu,+Palibe aliyense amene wachita zinthu zofanana ndi zimene inu mwachita.+ Salimo 89:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndi ndani kumwamba amene angafanane ndi Yehova?+ Ndi ndani pakati pa ana a Mulungu+ amene ndi wofanana ndi Yehova?
35 Inuyo mwasonyezedwa zinthu zimenezi kuti mudziwe kuti Yehova ndi Mulungu woona.+ Palibenso Mulungu wina kupatulapo iyeyo.+
8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu,+Palibe aliyense amene wachita zinthu zofanana ndi zimene inu mwachita.+
6 Ndi ndani kumwamba amene angafanane ndi Yehova?+ Ndi ndani pakati pa ana a Mulungu+ amene ndi wofanana ndi Yehova?