Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Samueli 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • 1 Samueli 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pa nthawiyi Eli anali atakalamba kwambiri koma anamva zonse zimene ana ake ankachitira+ Aisiraeli onse. Anamvanso kuti ankagona ndi akazi amene ankatumikira pakhomo la chihema chokumanako.+

  • 1 Samueli 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Munthu amene anabwera ndi uthengayo anati: “Aisiraeli athawa Afilisiti, ndipo agonjetsedwa koopsa.+ Ana anunso awiri, Hofeni ndi Pinihasi, aphedwa.+ Komanso Likasa la Mulungu woona lalandidwa.”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani