-
1 Samueli 15:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Koma Samueli anamuyankha kuti: “Sindibwerera nawe chifukwa wakana mawu a Yehova, ndipo Yehova wakukana kuti upitirize kukhala mfumu ya Isiraeli.”+
-