1 Samueli 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Sauli anachita mantha ndi Davide chifukwa Yehova anali ndi Davideyo,+ koma Sauliyo anali atamʼchokera.+
12 Ndiyeno Sauli anachita mantha ndi Davide chifukwa Yehova anali ndi Davideyo,+ koma Sauliyo anali atamʼchokera.+