Genesis 21:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Samueli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anadzuka mʼmawa ndipo atalambira Yehova anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona ndi mkazi wake Hana ndipo Yehova anamukumbukira.+
19 Kenako anadzuka mʼmawa ndipo atalambira Yehova anabwerera kunyumba kwawo ku Rama.+ Ndiyeno Elikana anagona ndi mkazi wake Hana ndipo Yehova anamukumbukira.+