Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Samueli 20:28, 29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Yonatani anayankha Sauli kuti: “Davide anandichonderera kuti ndimulole kupita ku Betelehemu.+ 29 Anandiuza kuti, ‘Chonde ndilole ndipite chifukwa banja lathu likukapereka nsembe mumzinda wakwathu. Mchimwene wanga ndi amene wandiitanitsa. Choncho ngati ungandikomere mtima, ndilole ndipite ndikaone abale anga.’ Nʼchifukwa chake sanabwere kudzadya ndi mfumu.”

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani