1 Samueli 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Davide anali mwana wa Jese wa ku Efurata+ ku Betelehemu,+ ku Yuda. Jese+ anali ndi ana aamuna 8+ ndipo mʼmasiku a Sauli, Jese anali atakalamba.
12 Davide anali mwana wa Jese wa ku Efurata+ ku Betelehemu,+ ku Yuda. Jese+ anali ndi ana aamuna 8+ ndipo mʼmasiku a Sauli, Jese anali atakalamba.