-
1 Samueli 18:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kenako Sauli anaponya mkondowo+ ndipo mumtima mwake ankati: ‘Ndibaya Davide nʼkumukhomerera kukhoma!’ Koma Davide anazinda nʼkuthawa ndipo zimenezi zinachitika kawiri konse.
-
-
1 Samueli 19:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Sauli anafuna kubaya Davide ndi mkondo kuti amukhomerere kukhoma. Koma Davide anauzinda moti mkondowo unalasa khoma. Usiku umenewo Davide anathawa.
-