Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 16:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mwamuna aliyense pakati panu azikaonekera katatu pa chaka pamaso pa Yehova Mulungu wanu, pamalo amene Mulungu adzasankhe. Azikaonekera pa Chikondwerero cha Mkate Wopanda Zofufumitsa,+ Chikondwerero cha Masabata+ ndi pa Chikondwerero cha Misasa.+ Palibe aliyense wa iwo amene akuyenera kukaonekera kwa Yehova chimanjamanja.

  • 1 Samueli 2:18, 19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiyeno Samueli ankatumikira+ pamaso pa Yehova ndipo ankavala efodi wansalu,+ ngakhale kuti anali mwana. 19 Komanso chaka chilichonse amayi ake ankamusokera kamkanjo kodula manja. Iwo ankamupititsira kamalayako akapita ndi amuna awo kukapereka nsembe yapachaka.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani