-
Salimo 78:60, 61Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
61 Analola kuti adani atenge chizindikiro cha mphamvu zake,
Analola kuti ulemerero wake ukhale mʼmanja mwa adani.+
-