1 Mafumu 2:36, 37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mbiri 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako iwo anakachotsa maguwa ansembe amene anali mu Yerusalemu.+ Anachotsanso maguwa onse a nsembe zofukiza+ nʼkukawataya kuchigwa cha Kidironi. Yohane 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
14 Kenako iwo anakachotsa maguwa ansembe amene anali mu Yerusalemu.+ Anachotsanso maguwa onse a nsembe zofukiza+ nʼkukawataya kuchigwa cha Kidironi.