Salimo 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwaipatsa madalitso mpaka kalekale.+Mwaichititsa kuti ikhale yosangalala chifukwa muli nayo pafupi.*+ Salimo 72:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale,+Ndipo lipitirize kutchuka kwa nthawi zonse pamene dzuwa lidzakhalepo. Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.+Mitundu yonse ya anthu imutchule kuti ndi wosangalala.
6 Mwaipatsa madalitso mpaka kalekale.+Mwaichititsa kuti ikhale yosangalala chifukwa muli nayo pafupi.*+
17 Dzina lake likhalebe mpaka kalekale,+Ndipo lipitirize kutchuka kwa nthawi zonse pamene dzuwa lidzakhalepo. Ndipo kudzera mwa iye, anthu apeze madalitso.+Mitundu yonse ya anthu imutchule kuti ndi wosangalala.