Deuteronomo 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pangʼono.”+ Yoswa 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ chifukwa iweyo ndi amene utsogolere anthuwa kuti akatenge dziko limene ndinalumbira kwa makolo awo kuti ndidzawapatsa.+ 1 Mbiri 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
6 Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.+ Musawaope kapena kuchita nawo mantha,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akuyenda patsogolo panu. Iye sadzakutayani kapena kukusiyani ngakhale pangʼono.”+
6 Ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu,+ chifukwa iweyo ndi amene utsogolere anthuwa kuti akatenge dziko limene ndinalumbira kwa makolo awo kuti ndidzawapatsa.+