2 Samueli 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anamʼtengera pambali kugeti kuti alankhulane naye pa awiri. Koma kumeneko anamubaya pamimba moti anafa.+ Anamupha chifukwa choti anapha Asaheli, mchimwene wake wa Yowabuyo.+ 2 Samueli 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho Yowabu ndi mchimwene wake Abisai+ anapha Abineri+ chifukwa chakuti iye anapha Asaheli mchimwene wawo pa nkhondo+ ku Gibiyoni.
27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anamʼtengera pambali kugeti kuti alankhulane naye pa awiri. Koma kumeneko anamubaya pamimba moti anafa.+ Anamupha chifukwa choti anapha Asaheli, mchimwene wake wa Yowabuyo.+
30 Choncho Yowabu ndi mchimwene wake Abisai+ anapha Abineri+ chifukwa chakuti iye anapha Asaheli mchimwene wawo pa nkhondo+ ku Gibiyoni.