-
2 Samueli 3:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Davide atamva zimenezi, ananena kuti: “Yehova akudziwa kuti ineyo ndi ufumu wanga tilibe mlandu wa magazi+ a Abineri mwana wa Nera mpaka kalekale.
-