Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Samueli 17:27-29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Davide atangofika ku Mahanaimu, Sobi mwana wamwamuna wa Nahasi wochokera ku Raba+ mzinda wa Aamoni, Makiri+ mwana wa Amiyeli wochokera ku Lo-debara komanso Barizilai+ wa ku Giliyadi wochokera ku Rogelimu, 28 anabweretsa mabedi, mabeseni, miphika, tirigu, balere, ufa, nyemba zikuluzikulu, mphodza, mbewu zina zokazinga, 29 uchi, nkhosa, bata ndiponso tchizi.* Anabweretsa zinthu zimenezi kuti Davide ndi anthu onse amene anali naye adye.+ Iwo ankati: “Anthuwa ali mʼchipululu ndipo ali ndi njala, ali ndi ludzu komanso atopa.”+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani