2 Samueli 5:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Davide anakhala mfumu ali ndi zaka 30 ndipo analamulira kwa zaka 40.+ 5 Ku Heburoni anakhala mfumu ya Yuda kwa zaka 7 ndi miyezi 6. Ku Yerusalemu+ analamulira Isiraeli yense ndi Yuda kwa zaka 33.
4 Davide anakhala mfumu ali ndi zaka 30 ndipo analamulira kwa zaka 40.+ 5 Ku Heburoni anakhala mfumu ya Yuda kwa zaka 7 ndi miyezi 6. Ku Yerusalemu+ analamulira Isiraeli yense ndi Yuda kwa zaka 33.