-
1 Samueli 22:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma mwana mmodzi wamwamuna wa Ahimeleki, mwana wa Ahitubu, dzina lake Abiyatara+ anapulumuka ndipo anathawa nʼkutsatira Davide.
-