-
Yoswa 21:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+
-
-
Yoswa 21:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Anatoti+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Alimoni ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.
-