-
1 Mafumu 18:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndipo pamene Yezebeli+ ankapha aneneri a Yehova, Obadiya anatenga aneneri 100 nʼkuwagawa mʼmagulu awiri, gulu lililonse aneneri 50. Atatero anakawabisa kuphanga nʼkumawapatsa chakudya ndi madzi.)
-