2 Samueli 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mlandu umenewu ubwerere pamutu pa Yowabu+ ndi anthu onse a nyumba ya bambo ake. Mʼnyumba ya Yowabu musadzasowe mwamuna wa nthenda yakukha kumaliseche,+ wakhate,+ wogwira ntchito yowomba nsalu,* wophedwa ndi lupanga kapena wosowa chakudya!”+
29 Mlandu umenewu ubwerere pamutu pa Yowabu+ ndi anthu onse a nyumba ya bambo ake. Mʼnyumba ya Yowabu musadzasowe mwamuna wa nthenda yakukha kumaliseche,+ wakhate,+ wogwira ntchito yowomba nsalu,* wophedwa ndi lupanga kapena wosowa chakudya!”+