-
1 Samueli 2:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Kenako ndidzasankha wansembe wanga wokhulupirika.+ Ameneyu adzachita mogwirizana ndi zimene mtima wanga ukufuna. Ndidzamʼmangira nyumba yokhalitsa, ndipo adzatumikira wodzozedwa wanga monga wansembe nthawi zonse.
-
-
1 Mbiri 6:53Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
53 Ahitubu anabereka Zadoki+ ndipo Zadoki anabereka Ahimazi.
-