Maliro 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Azimayi amene amakhala achifundo, aphika ana awo ndi manja awo.+ Anawo akhala chakudya chawo pa nthawi yachisoni pamene mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+
10 Azimayi amene amakhala achifundo, aphika ana awo ndi manja awo.+ Anawo akhala chakudya chawo pa nthawi yachisoni pamene mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+