2 Samueli 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Davide anayamba kukhala mʼmalo omwe anali mumpanda wolimba kwambiri, ndipo ankadziwika kuti* Mzinda wa Davide. Iye anayamba kumanga malo onsewo kuyambira ku Chimulu cha Dothi*+ mpaka mkati.+ 2 Mbiri 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mbiri 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
9 Kenako Davide anayamba kukhala mʼmalo omwe anali mumpanda wolimba kwambiri, ndipo ankadziwika kuti* Mzinda wa Davide. Iye anayamba kumanga malo onsewo kuyambira ku Chimulu cha Dothi*+ mpaka mkati.+