-
1 Mbiri 6:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Awa ndi anthu amene Davide anawapatsa udindo wotsogolera kuimba panyumba ya Yehova ataikapo Likasa.+
-
-
1 Mbiri 6:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Mʼbale wake Asafu+ ankaima kumanja kwake. Asafu anali mwana wa Berekiya, Berekiya anali mwana wa Simeya,
-