Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mbiri 16:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Iwowa anali limodzi ndi Hemani ndi Yedutuni+ ndiponso amuna onse amene anawasankha mochita kuwatchula mayina kuti azithokoza Yehova,+ chifukwa “chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.”+

  • 1 Mbiri 25:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • 1 Mbiri 25:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ana onsewa ankayangʼaniridwa ndi bambo awo poimba nyimbo panyumba ya Yehova. Ankaimba nyimbozo ndi zinganga, zoimbira za zingwe ndi azeze,+ potumikira panyumba ya Mulungu woona.

      Koma Asafu, Yedutuni ndi Hemani ankayangʼaniridwa ndi mfumu.

  • 1 Mbiri 25:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kwa Yedutuni,+ anatengako ana ake awa: Gedaliya, Zeri, Yesaiya, Simeyi, Hasabiya ndi Matitiya,+ onse pamodzi analipo 6. Iwowa ankayangʼaniridwa ndi Yedutuni bambo awo, amene ankalosera ndi zeze ndipo ankayamika ndi kutamanda Yehova.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani