-
1 Mafumu 8:54Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
54 Solomo atamaliza kupemphera kwa Yehova pemphero lonseli ndiponso kupempha chifundo, anachoka patsogolo pa guwa lansembe la Yehova, chifukwa nthawi yonseyi anali atagwada nʼkukweza manja ake mʼmwamba.+
-