-
2 Mbiri 2:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndipo ndani angathe kumangira Mulunguyo nyumba? Chifukwa kumwamba, ngakhalenso kumwamba kwa kumwamba, nʼkosakwanira kuti akhaleko.+ Ndiye ine ndine ndani kuti ndimumangire nyumba, kupatulapo yoperekeramo nsembe pamaso pake?
-