Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Levitiko 26:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma ngati simudzandimvera kapena kutsatira malamulo onsewa,+

  • Levitiko 26:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ine ndidzakukanani, ndipo adani anu adzakugonjetsani+ ndi kukuponderezani,+ moti muzidzathawa popanda munthu wokuthamangitsani.+

  • Yoswa 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pepanitu Yehova, ndingatinso chiyani nanga, poti Isiraeli wathawa pamaso pa adani ake?

  • Yoswa 7:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Aisiraeli achimwa ndiponso aphwanya pangano+ limene ndinawalamula kuti alisunge. Iwo atenga zina mwa zinthu zoyenera kuwonongedwa.+ Aba+ zinthuzo ndi kuzibisa pakati pa katundu wawo.+

  • Oweruza 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli, moti anawapereka mʼmanja mwa adani amene anawaukira nʼkutenga zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kulimbana nawo.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani