Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Levitiko 26:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma ngati simudzandimvera kapena kutsatira malamulo onsewa,+

  • Levitiko 26:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Deuteronomo 28:21, 22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yehova adzachititsa kuti matenda akukakamireni mpaka atakufafanizani mʼdziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu.+ 22 Yehova adzakulangani ndi chifuwa chachikulu, kutentha kwa thupi koopsa,+ kutupa, nyengo yotentha,* lupanga,+ mphepo yotentha yowononga mbewu ndi matenda a mbewu.+ Zimenezi zidzakuvutitsani mpaka mutatheratu.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani