-
Hagai 2:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ine ndinakulangani ndipo ndinawononga ntchito za manja anu pobweretsa mphepo yotentha, matenda a mbewu a chuku+ ndi matalala, koma palibe aliyense amene anabwerera kwa ine,’ watero Yehova.
-