Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ekisodo 35:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • 1 Mbiri 29:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Anthuwo anasangalala chifukwa cha nsembe zaufulu zimene anapereka, chifukwa anapereka nsembezo kwa Yehova ndi mtima wonse.+ Nayenso Mfumu Davide anasangalala kwambiri.

  • Ezara 7:14-16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwe watumizidwa ndi mfumu komanso alangizi ake 7 kuti ukafufuze ngati anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu akutsatira Chilamulo cha Mulungu wako, chimene uli nacho.* 15 Utenge siliva ndi golide zimene mfumu ndi alangizi ake apereka mwakufuna kwawo kwa Mulungu wa Isiraeli, amene amakhala ku Yerusalemu. 16 Utengenso siliva ndi golide yense amene ulandire* mʼchigawo chonse cha Babulo, limodzi ndi mphatso za anthu komanso za ansembe omwe akupereka mwakufuna kwawo kunyumba ya Mulungu wawo, yomwe ili ku Yerusalemu.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani