Esitere 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mfumuyi inkakhala pampando wake mʼnyumba yachifumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani.*+ Esitere 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Danieli 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikuona masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili kunyumba yachifumu* ku Susani,+ imene ili mʼchigawo cha Elamu.+ Ndinaona masomphenyawa kuti ndinali mʼmphepete mwa mtsinje wa Ulai.
2 mfumuyi inkakhala pampando wake mʼnyumba yachifumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani.*+
2 Ndikuona masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili kunyumba yachifumu* ku Susani,+ imene ili mʼchigawo cha Elamu.+ Ndinaona masomphenyawa kuti ndinali mʼmphepete mwa mtsinje wa Ulai.