Nehemiya 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Nehemiya 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yoyada mwana wa Paseya, komanso Mesulamu mwana wa Besodeya, anakonza Geti la Mzinda Wakale.+ Iwo analipangira felemu lamatabwa nʼkuika zitseko, anamphatika* ndi mipiringidzo. Nehemiya 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Hanuni ndi anthu a ku Zanowa+ anakonza Geti la Kuchigwa.+ Iwo analikonza nʼkuika zitseko, anamphatika ndi mipiringidzo. Anakonzanso mpandawo mikono 1,000* mpaka kukafika ku Geti la Milu ya Phulusa.+
6 Yoyada mwana wa Paseya, komanso Mesulamu mwana wa Besodeya, anakonza Geti la Mzinda Wakale.+ Iwo analipangira felemu lamatabwa nʼkuika zitseko, anamphatika* ndi mipiringidzo.
13 Hanuni ndi anthu a ku Zanowa+ anakonza Geti la Kuchigwa.+ Iwo analikonza nʼkuika zitseko, anamphatika ndi mipiringidzo. Anakonzanso mpandawo mikono 1,000* mpaka kukafika ku Geti la Milu ya Phulusa.+