-
Nehemiya 6:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 nthawi yomweyo Sanibalati ndi Gesemu ananditumizira uthenga wakuti: “Bwera tidzapangane nthawi yoti tikakumane mʼmudzi wina mʼchigwa cha Ono.”+ Koma ankandikonzera chiwembu.
-
-
Nehemiya 11:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 ku Lodi ndiponso ku Ono,+ chigwa cha amisiri.
-