-
Deuteronomo 4:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Anakuchititsani kuti mumve mawu ake kuchokera kumwamba nʼcholinga chakuti akulangizeni kuti muzimumvera. Padziko lapansi pano, iye anakuchititsani kuti muone moto waukulu, ndipo munamva mawu ake kuchokera pamotowo.+
-