-
Deuteronomo 18:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 “Alevi omwe ndi ansembe, komanso fuko lonse la Levi, sadzapatsidwa gawo kapena cholowa pakati pa Aisiraeli. Iwo azidzadya nsembe zowotcha pamoto zoperekedwa kwa Yehova, zomwe ndi cholowa chake.+
-
-
Deuteronomo 18:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Aziperekanso kwa wansembe mbewu zawo zoyambirira kucha, vinyo wawo watsopano, mafuta awo ndi ubweya wa nkhosa zawo umene ameta moyambirira.+
-